1 Akorinto 12:26 BL92

26 Ndipocingakhale ciwalo cimodzi cimva cowawa, ziwalo zonse zimva pamodzi; cingakhale cimodzi cilemekezedwa, ziwalo zonse zikondwera naco pamodzi,

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 12

Onani 1 Akorinto 12:26 nkhani