1 Akorinto 12:28 BL92

28 Ndipotu Mulunguanailea ena m'Eklesia, poyamba arumwi, aciwiri aneneri, acitatu aphunzitsi, pamenepo zozizwa, pomwepo mphatso zamaciritso, mathandizo, maweruziro, malilime a mitundu mitundu.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 12

Onani 1 Akorinto 12:28 nkhani