1 Akorinto 12:3 BL92

3 Cifukwa cace ndikuuzani inu, kuti palibe munthu wakulankhula mwa Mzimu wa Mulungu, anena, Yesu ngwotembereredwa; ndipo palibe wina akhoza kunena, Yew ali Ambuye, koma mwa Mzimu Woyera.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 12

Onani 1 Akorinto 12:3 nkhani