5 Ndipo ndifuna inu nonse mula'nkhule malilime, koma makamaka kuti mukanenere; ndipo wakunenera aposa wakulankhula malilime, akapanda kumasulira, kuti Mpingo ukalandire comangirira.
Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 14
Onani 1 Akorinto 14:5 nkhani