1 Akorinto 14:9 BL92

9 Momwemonso inu ngati mwa lilime simupereka mau omveka bwino, kudzazindikirika bwanji cimene cilankhulidwa? Pakuti mudzakhala olankhula kumlengalenga.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 14

Onani 1 Akorinto 14:9 nkhani