1 Akorinto 15:39 BL92

39 Nyama yonse siiri imodzimodzi; koma yinandi Ya anthu, ndi yina ndiyo nyama ya zoweta, ndi yina ndiyo nyama ya mbalame, ndi yina ya nsomba.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 15

Onani 1 Akorinto 15:39 nkhani