1 Akorinto 3:10 BL92

10 Monga mwa cisomo ca Mulungu cidapatsidwa kwa ine, ngati mwini mamangidwe waluso, ndinaika maziko, koma wina amangapo. Koma yense ayang'anire umo amangira pamenepo.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 3

Onani 1 Akorinto 3:10 nkhani