1 Akorinto 6:7 BL92

7 Koma pamenepo pali cosowa konse konse mwa inu, kuti muli nayo mirandu wina ndi mnzace. Cifukwa ninji simusankhula kulola kuipsidwa? simusankhula cifukwa ninji kulolakunyengedwa?

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 6

Onani 1 Akorinto 6:7 nkhani