22 Pakuti iye amene anaitanidwa mwa Ambuye, pokhala ali kapolo, ali mfulu ya Ambuye: momwemonso woitanidwayo, pokhala ali mfulu, ali kapolo wa Kristu.
Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 7
Onani 1 Akorinto 7:22 nkhani