1 Akorinto 7:28 BL92

28 Koma ungakhale ukwatira, sunacimwa; ndipo ngati namwali akwatiwa, sanacimwa. Koma otere adzakhala naco cisautso m'thupi, ndipo ndikulekani.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 7

Onani 1 Akorinto 7:28 nkhani