30 ndi iwo akulira, monga ngati salira, ndi iwo akukondwera, monga ngati sakondwera; ndi iwo akugula monga ngati alibe kanthu;
Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 7
Onani 1 Akorinto 7:30 nkhani