1 Akorinto 7:5 BL92

5 Musakanizana, koma ndi kubvomerezana kwanu ndiko, kwa nthawi, kuti mukadzipereke kwa kupemphera, nimukakhalenso pamodzi, kuti Satana angakuyeseni, cifukwa ca kusadziletsa kwanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 7

Onani 1 Akorinto 7:5 nkhani