1 Akorinto 7:7 BL92

7 Koma mwenzi anthu onse akadakhala monga momwe ndiri ine ndekha. Koma munthu yense ali nayo mphatso yace ya iye yekha kwa Mulungu, wina cakuti, wina cakuti.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 7

Onani 1 Akorinto 7:7 nkhani