1 Akorinto 9:12 BL92

12 Ngati ena ali nao ulamuliro umene pa inu, si ife nanga koposa? Koma sitinacita nao ulamuliro umene; koma timalola zonse, kuti tingacite cocedwetsa kwa Uthenga Wabwino wa Kristu,

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 9

Onani 1 Akorinto 9:12 nkhani