1 Akorinto 9:20 BL92

20 Ndipo kwa Ayuda ndinakhala monga Myuda, kuti ndipindule Ayuda; kwa iwo omvera lamulo monga womvera lamulo, ngakhale sindinakhala ndekha womvera lamulo, kuti ndipindule iwo omvera malamulo;

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 9

Onani 1 Akorinto 9:20 nkhani