2 Akorinto 1:17 BL92

17 Pamenepo, pakufuna cimene, kodi ndinacitapo kosinthasintha? Kapena zimene nditsimikiza mtima kodi ndizitsimikiza mtima monga mwa thupi? Kuti pa ine pakhale eya, eya, ndi iai, iai?

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 1

Onani 2 Akorinto 1:17 nkhani