2 Akorinto 10:1 BL92

1 Koma ine ndekha Paulo, ndidandaulira inu mwa kufatsa ndi ulere wa Kristu, ine amene pamaso panu ndikhala wodzicepetsa pakati pa inu, koma pokhala kwina ine ndilimbika mtima kwa inu;

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 10

Onani 2 Akorinto 10:1 nkhani