2 Akorinto 10:2 BL92

2 koma ndipempha kuti pokhala ndiri pomwepo, ndisalimbike mtima ndi kulimbika kumene ndiyesa kulimbika nako pa ena, amene atiyesera ife monga ngati tirikuyendayenda monga mwa thupi,

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 10

Onani 2 Akorinto 10:2 nkhani