11 Wotereyo ayese ici kuti monga tiri ife ndi mau mwa akalata, pokhala palibe ife, tiri oterenso m'macitidwe pokhala tiri pomwepo.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 10
Onani 2 Akorinto 10:11 nkhani