2 Akorinto 10:12 BL92

12 Pakuti sitilimba mtima kudziwerenga, kapena kudzilinganiza tokha ndi ena a iwo amene adzibvomeretsa okha; koma iwowa, podziyesera okha ndi iwo okha, ndi kudzilinganiza okha ndi iwookha, alibe nzeru.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 10

Onani 2 Akorinto 10:12 nkhani