13 Koma ife sitidzadzitamandira popitirira muyeso, koma monga mwa muyeso wa cilekelezero cimene Mulungu anatigawira muyeso, kufikira ngakhale kwa inunso.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 10
Onani 2 Akorinto 10:13 nkhani