2 Akorinto 10:15 BL92

15 osadzitamandira popitirira muyeso mwa macititso a ena; koma tiri naco ciyembekezo kuti pakukula cikhulupiriro canu, tidzakulitsidwa mwa inu monga mwa cilekezero cathu kwa kucurukira,

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 10

Onani 2 Akorinto 10:15 nkhani