13 Pakuti kuli ciani cimene munacepetsedwa naco ndi Mipingo yotsala yina, agati, si ici kuti ine ndekha sindirasaukitsa inu? Ndikhululukireni oipa ici.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 12
Onani 2 Akorinto 12:13 nkhani