14 Taonani, nthawi yaitatu iyi ndapukwa ine kudza kwa nu, ndipo sindidzakusaukitsani; pakuti sindifuna zanu, koma inu; cakuti ana sayenera kuunjikira atate adi amai, koma atate ndi amai kumjikira ana.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 12
Onani 2 Akorinto 12:14 nkhani