10 Koma amene mumkhululukira kanthu, inenso nditero naye; pakuti cimene ndakhululukira inenso, ngati ndakhululukira kanthu, ndacicita cifukwa ca inu, pamasopa Kristu;
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 2
Onani 2 Akorinto 2:10 nkhani