15 Pakuti zonsezi nza kwa inu, kuti cisomoco, cocurukitsidwa mwa unyinjiwo, cicurukitsire ciyamiko ku ulemerero wa Mulungu.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 4
Onani 2 Akorinto 4:15 nkhani