17 Pakuti cisautso cathu copepuka ca kanthawi citicitira ife kulemera koposa kwakukuru ndi kosatha kwa ulemerero;
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 4
Onani 2 Akorinto 4:17 nkhani