18 popeza sitipenyerera zinthu zooneka, koma zinthu zosaoneka; pakuti zinthu zooneka ziri za nthawi, koma zinthu zosaoneka ziri zosatha.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 4
Onani 2 Akorinto 4:18 nkhani