1 Pakuti tidziwa kuti ngati nyumba ya pansi pano ya msasa wathu ipasuka, tiri naco cimango ca kwa Mulungu, ndiyo nyumba yosamangidwa ndi manja, yosatha, m'Mwamba.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 5
Onani 2 Akorinto 5:1 nkhani