2 Akorinto 5:16 BL92

16 Kotero kuti ife sitidziwanso munthu tsopano monga mwa thupi; ndipo ngati tazindikira Kristu monga mwa thupi, koma tsopano sitimzindikiranso motero.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 5

Onani 2 Akorinto 5:16 nkhani