2 Akorinto 7:8 BL92

8 Kuti ngakhale ndakumvetsani cisoni ndi kalata uja, sindiwawapo mtima, ndingakhale ndinawawa mtima; pakuti ndiona kuti kalata uja anakumvetsani cisoni, ngakhale kwa nthawi yokha.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 7

Onani 2 Akorinto 7:8 nkhani