2 Akorinto 8:22 BL92

22 Ndipo tinatumiza mbale wathu awaperekeze iwo, amene tamtsimikizirakawiri kawiri ali wakhama m'zinthu zambiri, koma tsopano wa khama loposatu ndi kulimbika kwakukuru kumene ali nako kwa inu,

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 8

Onani 2 Akorinto 8:22 nkhani