2 Akorinto 8:9 BL92

9 Pakuti mudziwa cisomo ca Ambuye wathu Yesu Kristu, kuti, cifukwa ca inu anakhala wosauka, angakhale anali wolemera, kuti inu ndi kusauka kwace mukakhale olemera.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 8

Onani 2 Akorinto 8:9 nkhani