1 Akorinto 1:25 BL92

25 Cifukwa kuti copusa ca Mulungu ciposa anthu ndi nzeru zao; ndipo cofoka ca Mulunguciposa anthu ndi mphamvu yao.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 1

Onani 1 Akorinto 1:25 nkhani