1 Akorinto 16:11 BL92

11 cifukwa cace munthu asampeputse, Koma mumperekeze mumtendere, kuti akadze: kwa ine; pakuti ndimuyembekezera pamodzi ndi abale,

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 16

Onani 1 Akorinto 16:11 nkhani