1 Akorinto 16:12 BL92

12 Koma za Apolo, mbaleyo, ndamuumiriza iye, adze kwa inu pamodzi ndi abale; ndipo sicinali cifuniro cace kuti adze tsopano, koma adzafika pameneaona nthawi.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 16

Onani 1 Akorinto 16:12 nkhani