1 Akorinto 2:11 BL92

11 Pakuti ndani wa anthu adziwa za munthu, koma mzimu wa munthuyu uli mwa iye? momwemonso za Mulungu palibe wina azidziwa, koma Mzimu wa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 2

Onani 1 Akorinto 2:11 nkhani