1 Akorinto 2:12 BL92

12 Koma sitinalandira ife mzimu wa dziko lapansi, koma Mzimu wa kwa Mulungu, kuti tikadziwe zimene zipatsidwa kwa ife ndi Mulungu kwaufulu.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 2

Onani 1 Akorinto 2:12 nkhani