1 Akorinto 7:40 BL92

40 Koma akhala wokondwera koposa ngati akhala monga momwe ali, monga mwa kuyesa kwanga; ndipo ndiganiza kuti inenso ndiri naye Mzimu wa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 7

Onani 1 Akorinto 7:40 nkhani