1 Koma za zoperekedwa nsembe kwa mafano: Tidziwa kuti tid naco cidziwitso tonse. Cidziwitso citukumula, koma cikondicimangirira.
Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 8
Onani 1 Akorinto 8:1 nkhani