10 Pakuti wina akaona iwe amene uli naco cidziwitso, ulikukhala pacakudya m'kacisi wa fano, kodi cikumbu mtima cace, popeza ali wofoka, sieidzalimbika kudya zoperekedwa nsembe kwa mafano?
Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 8
Onani 1 Akorinto 8:10 nkhani