1 Akorinto 8:11 BL92

11 Pakuti mwa cidziwitso cako wofokayo atayika, ndiye mbale amene Kristu anamfera.

Werengani mutu wathunthu 1 Akorinto 8

Onani 1 Akorinto 8:11 nkhani