2 Pakuti ndicita nsanje pa inu ndi nsanje ya Mulungu; pakuti ndinakupalitsani ubwenzi mwamuna mmodzi, kuti ndikalangize inu ngati namwali woyera mtima kwa Kristu.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 11
Onani 2 Akorinto 11:2 nkhani