3 Koma ndiopa, kuti pena, monga njoka inanyenga Heva ndi kucenjerera kwace, maganizo anu angaipsidwe kusiyana nako kuona mtima ndi kuyera mtima ziri kwa Kristu.
Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 11
Onani 2 Akorinto 11:3 nkhani