Aroma 11:18 BL92

18 usadzitama iwe wekha pa nthambizo: koma ngati udzitama wekha, suli iwe amene unyamula muzu, ai, koma muzu ukunyamula iwetu.

Werengani mutu wathunthu Aroma 11

Onani Aroma 11:18 nkhani