Aroma 11:2 BL92

2 Mulungu sanataya anthu ace amene iye anawadziwiratu, Kapena simudziwa kodi cimene lembo linena za Eliya? kuti anaumirira Mulungu poneneza Israyeli, kuti,

Werengani mutu wathunthu Aroma 11

Onani Aroma 11:2 nkhani