33 Ha! kuya kwace kwa kulemera ndi kwa nzeru ndi kwa kudziwa kwace kwa Mulungu! 4 Osasanthulikadi maweruzo ace, ndi njira zace nzosalondoleka!
Werengani mutu wathunthu Aroma 11
Onani Aroma 11:33 nkhani