36 Cifukwa 7 zinthu zonse zicokera kwa iye, zicitika mwa iye, ndi kufikira kwa iye. 8 K wa Iyeyo ukhale ulemerero ku nthawi zonse. Amen.
Werengani mutu wathunthu Aroma 11
Onani Aroma 11:36 nkhani