1 Anthu onse amvere maulamuliro a akulu; pakuti palibe ulamuliro wina koma wocokera kwa Mulungu; ndipo iwo amene alipo aikidwa ndi Mulungu.
Werengani mutu wathunthu Aroma 13
Onani Aroma 13:1 nkhani