21 Kuli kwabwino kusadya nyama, kapena kusamwa vinyo, kapena kusacita cinthu ciri conse cakukhumudwitsa mbale wako.
Werengani mutu wathunthu Aroma 14
Onani Aroma 14:21 nkhani